๐๐๐๐๐'๐ ๐๐๐
To teach something that can help someone
27/08/2022
๐ ๐๐ฎ๐ป๐ฎ ๐๐ฎ ๐ป๐๐ฎ๐ป๐ด๐ฎ...
Part..01
Dzina langa ndine Yahaya ndinali ndi nzanga yemwe tinamphunzira limodzi school kalero.Kunena zoona zangayo school anafika nayo patali ndithu moti anapeza ntchito ngati mloya. Dzina la nzangayo ndi Henwood. Kumbali ya ine school ndidayikanika chifukwa ndidatamangila kupita ku jonz nthawi imeneyo.Ndi kumvuta kwa zinthu ndidabwerako ku south africa pa dipoti.Ndinalibe poyambila ngakhale ndalama yoti mwina nditha kuyambila business. Kufikira tsiku lina ndidakumana ndi nzanga Henwood, kunena zoona ndidamusilira ngakhale mene amaonekera zimaonetsa kuti ndalama zidamuyanja ndithu.Tidacheza nkhani izi ndi izo kupatikiza apo adandiuza kuti adakwatira ndipo ali ndi mwana modzi wa mkazi.kumbali ya ine ndidali ndizanakwatire poganizira ndi mavuto omwe ndidali nawo. Ndidamudandaulira mene mavuto ndidali kukumana nawo.Adandiuza kuti ndizadandaule andithandiza ndithu.nditamva izi ndidasangalala kwambili ndipo adandiuza kuti lamulungu azabwera kuzanditenga kupita nane kwawo koma choyamba ayambe akambilana kaye ndi kazi wake.Macheza athu tsiku limeneri anali bwino kwambili.Ndipo ndidamupeleketsa pomwe amakakwera galimoto yake ya range lover.Utsiku wa tsiku limenero mtulo ndinabwera poganizira kuti ndakumana ndi munthu woti andithandiza.Loweruka lidafika ndipo ndidali nditakhala pa khonde pa kanyumba yanga.Ndidaona galimoto ya range lover ikubwera poteropo ndipo mtima wanga unali ndi chisangalaro kwambili.mzanga uja adatuluka galimoto ndipo ndidamulonjera ndithu. Adandiuza kuti kazi wake alibe nazo mvuto nditha kupita kukakhala nawo.Kunena zoona ndidali ndi chisangalaro mu mtima mwanga kotero ndidalowa nyumba kukalongetsa nyangwita.idali 10:25 nthawi yomwe tidanyamuka kupita kunyumba kwawo.
Nditafika analoweza galimoto yake ku mpanda.Ndipo tidalowa nyumba mwake momwe tidakumana ndi kazi wake yemwe adatilonjera mwasangala. Kunena zoona henwood amadziwa mkazi. anali wa oyera ngati kalade,wa ma hip komanso ndi nkhope yotenga mtima ndi timano take toyera akamayankhula ngati azasiye.Anabwereza zakumwa zoti timwe.Ndipo ndidamuyamikira nzangoyo kuti adali ndi kazi waulemu.Titamaliza kumwa adanditenga kupita nane kunyuma ya alendo.Ndipo adandiuza kuti chili chonse chomwe ndikufuna azindipangila ku akundiyang'anira ntchito yabwino.poti iye ku mawa amapita ku ntchito komanso kazi wake ali pa ntchito ngati wapolisi. Moti pakomopo nthawi zambili pamakhala mwana wawo yekha akati wabwerako ku school.idakwana nthawi 02:20 pomwe padatulukira mwana wake wa kazi. kunena zoona mwana wake adali owala kutengela mayi ake adali oyera. Akamayenda ma hip ake ngati akufuna kung'amba unform yomwe adamvala, adali onenepa bwino ndithu komanso wa medium sadali wa mtali kapena wa mfupi ndipo myendo yake yokhala ngati ya matewe koma ayi. Mtima wa ngati nditamuona ndidamusilira koopsa moti sindimaonezera kuopa kunditulukira.Nzanga uja adandipanga ine introduce kwa mwana wake uja. Ndipo mwana wake uja adandilonjera.Utsiku wa tsiku limenero ndidali ndi kuvina mkati mwa nyumba yomwe adandipatsa kuti ndizikhalamo chili chisangalaro.Mawa ku m'mawa zanga uja ndi kazi wake adapita ku ntchito mwa nthawi zonse momwe amachitira nthawi zonse adandizatsika.Sipanatenge nthawi ndamuona mwawo wa mkazi uja naye ali mu unform,adandipatsa moni kenako kutenga chikwama chake ulendo wa ku school kunena zoona ndidali naye chidwi kwambili. Pakomopo ndidakhala ndekha kenaka ndayatsa tv yomwe idali chipinda muja kumaonera ma movies.Ndidamva kukoma ndithu tsiku limeneri moti ndimatenga chomwe ndachifuna mu firiji ndi kumamwa.Nthawi pomwe imati 02:25 ndidamva pa gate ngweem ndidaziwa kuti mwana wa nzanga uja ameneyo kubwerako ku school. ndidasusumira pa window adali yemweyodi akuchita kuyendetsa mbuyo ngati kulibe mawa. Ndipo mtima wanga udati katundu uja wafika tsopano.
๐ฉ๐๐ง๐ ๐๐ง๐ข ๐๐จ๐ฆ๐ฆ๐๐ง๐ญ ๐๐ง๐ ๐ฅ๐ข๐ค๐ ๐ค๐ฎ๐ญ๐ข ๐ข๐ฉ๐ข๐ญ๐ข๐ฅ๐ข๐ซ๐.
๐๐๐ง๐ ๐ ๐ฆ๐ฐ๐๐ฒ๐ข๐ฅ๐๐ง๐๐ข๐ซ๐ ๐ฆ๐ฐ๐๐ง๐ฃ๐ข ๐ข๐ฆ๐๐ง๐๐ฒ๐ข.
Ndi nkhani yabwino komanso muli phunziro.
pangani like ku page ya ๐ฌ๐๐๐๐'๐ ๐๐๐ kuti nkhani zonse muzitha kuwerenga mosatana bwino.
Cliquez ici pour rรฉclamer votre Listage Commercial.