Add your knowledge
We don't like bad language in this page only good ideas
Komatu koma ndikafuna kuchapa ndikhale ndi ndalama yosachepera k200 tifika nazo ku
Koma munthu ukapeza wachikondi eeeee umasangalala moposa muyezo ayi ndi chinthu chabwino kusiyana ndi kuba
Mwanva chani za zomwe zikuchitika MU dzikoli MU matsiku otsilidza
Surtu
Ngati lero sugwada pansi ndikupemphera utaya m'dalitso wako osayiwala kupemphera ukamagona thanks to all who loves God
Add your knowledge Send a message to learn more
Umphawi Ku Malawi sutithera chilichonse ndichobedwa palibe kuti ichi chokha ayi komatu koma eeeeee Amalawi ndikatundu omanga ndi mawaya lamba wachepa
03/10/2021
God loves everyone if we trust in him every thing will be better to our life
You are welcome both of you
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Website
Address
M 1
Blantyre
AD